Pular para o conteúdo
Publicidade

Matayo 6:31-33

NTNYBL2025 Nyanja

31 "Chimwecho, msadajhichaucha nimkamba, ‘Sitidye chiyani! Kapina sitimwe chiyani! Kapina sitivale chiyani!’ 32 Pakuti yameneyo yonjhe wandhu yao siamjhiwa Mnungu ajhichauchila yaya yonjhe. Atate wanu akumwamba ajhiwa kuti mfuna ivi vonjhe. 33 Chimwecho, ufuneni uti ufumu wa Mnungu ni kuchita yayo wayafuna Mnungu, ni iye siwakupacheni yaya yonjhe.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    31 Chifukwa chake musadere nkhawa ndi kuti, ‘Tidzadya chiyani?’ kapena ‘Tidzamwa chiyani?’ kapena ‘Tidzavala chiyani?’ 32 Pakuti anthu akunja amazifuna zinthu zonsezi ndipo Atate anu akumwamba adziwa kuti musowa zimenezi. 33 Koma muyambe mwafuna ufumu wake ndi chilungamo chake ndipo zinthu zonsezi zidzapatsidwa kwa inu.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.