9 Bwanji, kuli waliyonjhe pakati panu uyo mwana wake wakapembha bumunda siwamninghe mwala? 10 Kapina, wakampembha njhomba wampacha njoka? 11 Ngati anyiimwe woipa mujhiwa kwaapacha wana wanu vindhu vabwino, uzene Atate wanu akumwamba siwaapache vabwino anyiwajha ampembha."
Publicidade
Matayo 7:9-11
NTNYBL2025 Nyanja
Em outras traduções
- TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
9 "Ndani mwa inu, mwana wake akamupempha buledi amamupatsa mwala? 10 Kapena ngati mwana apempha nsomba, kodi amamupatsa njoka? 11 Tsono ngati inu woyipitsitsa mumadziwa kupatsa ana anu mphatso zabwino, nanga Atate anu akumwamba sadzapereka mphatso zabwino kwa iwo amene amupempha?
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.