Pular para o conteúdo
Publicidade

1 Coríntios 7

15 Nambho, wammuna kapina wamkazi siwadakhulupile wafuna kumsiya mnjake uyo wakhulupilila, chimwecho wachite chimwecho. Pakuchita chimwecho, wamkazi kapina wammuna wakhulupila siwamangika ndande Mnungu watitana tikhale ni umoyo wa mtendele. 16 Iwe wamkazi wamkhulupilila Yesu ujhiwa bwanji, ngati siumuombola mmunako? Kapina iwe wammuna ujhiwa bwanji ngati siumuombola mkazako?

Veja também