38 Pilato wadamkambila, "Zene nde chiyani?"
Yesu walamulidwa kufa
Pilato yapo wadakamba yameneyo, wadachotanjho Ayahudi kubwalo, wadakambila, "Ine sinidachione chilichonjhe icho walakwa mundhu uyu.