12 Nambho anyiyawo adamlandila, nikumkhulupilila mwadapacha nghongono za kukhala wana Amnungu, nde anyiwajha alikhulupilila jhina lawo, 13 anyiyawo abadwa asati kwa mwazi, kapina kwa kukonda kwa thupi au kukonda kwa mundhu, nambho Amnungu nde yawo adali Atate wao.