Pular para o conteúdo
Publicidade

João 20

Yesu wamtulukila Tomaso

24 Nambho Tomaso, uyo wamatanidwa Mawila mmojhi wa oyaluzidwa anyiwajha khumi ni awili, siwadali pamojhi nao yapo wadajha Yesu. 25 Ndiipo, oyaluzidwa wina adamkambila, "Taona Ambuye." Nambho iye wadaakambila, "Nikasiya kuona mawala ya mizumali mmanja mwake ni kubiza chala changa mmawala ya mizumaliyo ni kubiza jhanja langa mundhiti mwake, sinikhulupilila."

26 Chimwecho, pambuyo pa masiku nane oyaluzidwa adalinjho pamojhi mujha munyumba, ni Tomaso wadali pamojhi nao. Vicheko vidamangidwa ni kuima pakati pao wadakamba, "Mtendele ukhale kwanu!" 27 Ndiipo wadamkambila Tomaso, "Jhanacho chala chako upenye manja yanga, jhanalo jhanja lako ubize mundhiti mwanga. Msadakhaikila, nambho khulupilila!"

28 Tomaso wadayangha, "Ambuye wanga ni Amnungu wanga!"

29 Yesu wadammbila, "Bwanji unikhulupilila ndande waniona? Apachidwa mwawi anyiiwo sadanione, nambho akhulupilila."

Veja também