3 Yesu wadamuyangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kakawili siwakhoza kuuona Ufumu wa Amnungu."
4 Ndiipo Nikodemo wadamfunjha, "Mzee wakhoza bwanji kubadwanjho? Siwakhoze bwanji kulowa mmimba mwa amaye wake nikubaadwanjho?"
5 Yesu wadayangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kwa majhi ni Mzimu, siwakhoza kulowa mu Ufumu wa Amnungu