31 Ndhawi imweyo oyaluzidwa wake amampembelela Yesu, "Oyaluza, madyani ata pang’onope."
32 Ndiipo Yesu wadaakambila, "Ine nili ni chakudya icho simuchijhiwa."
33 Oyaluzidwa wake adamfunjha, "Bwanji, pali ni mundhu uyo wampelekela chakudya?"
34 Yesu wadayangha, "Chakudya changa nde ichi, kuchita icho wafuna uyo wanituma ni kuimaliza njhito yake.