27 Msadajhichaucha ndande ya chakudya icho chilula, nambho jhichaucheni ndande ya chakudya icho sichilula ndande ya umoyo wa muyaya. Mwana wa Adamu uyo Atate amchimikiza siwakupacheni chakudya chimenecho."
28 Ndiipo adamfunjha Yesu, "Tichite chiyani kuti tikhoze kuichita njhito ya Amnungu?"
29 Yesu wadayangha "Ino nde njhito iyo Amnungu afuna muichite, kumkhulupilila uyo amtuma."