42 "Nambho, mavuto yakhale kwa anyiimwe Afalisayo, pakuti chifuko simufuna kwachitila wina ubwino ni kumkonda Mnungu. Nambho, mumchochela Mnungu fungo limojhi pakati pamafungo khumi ya thelele, ni vindhu vokomecha thelele. Mufunika kwachitila wina bwino ni kumkonda Mnungu, pamojhi ni kuchocha fungo limojhi pakati pa mafungo khumi.