13 Mwachizulumukila gulu la lalikulu la atumiki akumwamba lidatulukila lili pamojhi ni achanjao atumiki wa kumwamba wa Mnungu, niamtamanda Mnungu niakamba,
14 "Ulemelelo ukhale kwa Mnungu wali kumwamba kupunda
ni pano pajhiko lapanjhi pakhale ni mtendele
kwa wandhu yawo waakonda!"