Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 22

42 "Atate, ngati ikhozekana, mavuto yaya yasadanipata, nambho osati ngati umo nifunila ine, nambho ikhale ngati umo mfunila imwe." 43 Pamwepo, atumiki akumwamba a Mnungu adamtulukila kuti amthile mtima. 44 Ni Yesu wali mkati mwa kupweteka kwakukulu, wadapembhela kupunda. Chitukuta chake chidali ngati mitondho ya mwazi iyo imasililika panjhi.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também