Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 18

Yani waliwamkulu pa Ufumu wa Mnungu

1 Ndhawi imeneyo oyaluzidwa adamchata Yesu, adaamfunjha, "Yani uyo wali wamkulu kupitilila wonjhe mu Ufumu wa kumwamba?"

2 Yesu wadamtana mwana wamng’ono ni kumwimika pakati pao, 3 Ndiipo wadaakambila, "Zene nikukambilani, ngati simng’anamuka ni kulingana ni wana waang’onoangono, simulowa mu Ufumu wa kumwamba. 4 Waliyonjhe uyo wajhichepecha ngati mwana uyu, nde uyo siwakhale wamkulu mu Ufumu wa kumwamba.

Veja também