13 Chilichonjhe icho simupembhe ngati umo nifunila sinichite, dala Atate apachidwe ulemelelo mkati mwa Mwana. 14 Mkanipembha chilichonjhe ngati umo nifunila, sinikuchitileni."
Yesu waahidi kumpeleka Mzimu woyela
15 "Ngati mnikonda malamulo yanga yawo nikupachani simuya chitile njhito. 16 Sinaapembhe Atate nawo sakupacheni Wakukuthandizani mwina, uyo siwakhale namwe muyaya.