8 Filipo wadamkambila Yesu, "Ambuye tilangizeni Atate, kwatu ikwana."
9 Yesu wadamkambila, "Filipo nakhala namwe ndhawi yonjheyi, ukali osanijhiwe? Uyo waniona ine waona Atate. Ukamba bwanji, ‘Tilangizeni Atate?’