Pular para o conteúdo
Publicidade

Yohana 14

9 Yesu wadamkambila, "Filipo nakhala namwe ndhawi yonjheyi, ukali osanijhiwe? Uyo waniona ine waona Atate. Ukamba bwanji, Tilangizeni Atate?10 Bwanji, siukhulupilila kuti ine nili mkati mwa Atate, ni Atate ali mkati mwanga? Mawu yayo nikukambilani osati kwa lamulo langa, Atate yawo alimkati mwanga achita njhito zao.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também