Pular para o conteúdo
Publicidade

João 19

4 Pilato wadatulukanjho kubwalo, wadaakambila, "Mjhiwe kuti ine sinidaone cholakwa chililonjhe kwake, chipano nimpeleka kwanu." 5 Chimwecho Yesu wadatuluka kubwalo wavala chisoti cha minga ni njhalu ya itali ya chifumu ya zambalau. Pilato wadamkambila, "Mundhu wanu yuno pano."

6 Ajhukulu waakulu ni alonda anyumba ya Amnungu yapo adamuona adakweza mvekelo, "Mpachikeni! Mpachikeni!"

Ndiipo Pilato wadaakambila, "Mtengeni mwachinawene, mkampachike ndande ine sinidaone cholakwa chilichonjhe cha kumlamula."

Veja também