17 Wadamfunjha kakatatu, "Simoni mwana wa Yohana! Bwanji, unikonda?"
Petulo wadadandaula kupunda ndande wadamfunjha katatu, "Unikonda?" Wadamkambila, "Ambuye, imwe mujhiwa yonjhe, mujhiwa kuti nikukondani."
Yesu wadamkambila, "Dyecha gulu la mbelele zanga.