Pular para o conteúdo
Publicidade

João 3

5 Yesu wadayangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kwa majhi ni Mzimu, siwakhoza kulowa mu Ufumu wa Amnungu 6 Mundhu wabadwa chithupi kwa atate wake ni amake, nambho wabadwa Chizimu kwa Mzimu woyela. 7 Siudadabwa pakuti nakukambila kuti lazima kubadwanjho.

Veja também