57 Ngati umo Atate yawo ali amoyo adanitumila, nane nili wamoyo kupitila iwo, chimwecho uyo waniidya ine siwakhale moyo kupitila ine. 58 Chino nde chakudya icho chachika kuchoka kumwamba, osati ngati mana iyo adadya azee wanu, ndiipo adamwalila. Uyo wakudya bumunda lino siwakhale moyo muyaya."