Pular para o conteúdo
Publicidade

João 8

10 Yesu yapo wadaima wadamfunjha wamkaziyo, "Alikuti wajha wandhu akupacha mlandhu? Palibe waliyonjhe uyo wakulamula?"

11 Wamkazi mmeneyo wadayangha, "Wakulu, palibe waliyonjhe!"

Ndiipo Yesu wadamkambila, "Ata ine sinikulamula. Mapita siudachitanjho machimo."

Veja também