2 Basi oyaluzidwa wake adamfunjha, "Oyaluza! Yani wachita machimo, mundhu uyu kapina obala wake, mbaka wabadwe osapenye?"
3 Yesu wadaayangha, "Wabadwa osapenye osati ndande ya machimo yake, kapina ya obala wake, wadabadwa chimwecho kuti mbhavu ya Amnungu iwoneke muumoyo wake.