11 Bwanji, ni tate yuti pakati panu uyo mwana wake wakampembha njhomba, wampacha njoka mmalo mwa njhomba? 12 Kapina mwana wakapembha zila wampache chipilili? 13 Chipano ngati anyiimwe, yawo muli wolakwa, mujhiwa kwapacha wana wanu vindhu vabwino, zenedi Atate wanu wakumwamba sayendekele kupunda kwapacha Mzimu Woyela yawo ampembha."