Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 2

10 Nambho mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadaakambila, "Msadaopa! Nakupelekelani uthenga wabwino uwo siwakondweleche kupunda wandhu wonjhe. 11 Pakuti lelo mmujhi wa Daudi wabadwa olamicha ndande yanu, iye nde Kilisito Ambuye. 12 Ichi nde chizindikilo chanu, simumkomane mwana wakhanda uyo wavekedwa matewela ni wagonekedwa mchidiku cho dyechela ng’ombe."

Veja também