34 Simiyoni wadaapacha mwawi, ni kumkambila Maliya make wa mwana, "Mwana uyu siwakhale chifuko cha khugwa ni kuomboka wandhu ambili mu Izilaeli. Iye siwakhale chizindikilo chochokela kwa Mnungu icho sichikanidwe ni wandhu ambili, 35 ni maganizo ya wandhu ambili siyaonekane padanga, ni iwe umwene wake siudandaule kupunda."