Yesu watengedwa kupita kumwamba
50 Ndiipo, Yesu wadaachogoza woyaluzidwa wake kupita mbaka mbhepete mwa mujhi wa Besaniya, pamenepo wadakweza manja yake ni kwapacha mwawi. 51 Yesu yapo wamapacha mwawi, wadatengedwa kumwamba ni kwasiya ni kupita kumwamba.