Mwali wa Yailo wahyukichidwa ni wamkazi walamichidwa
40 Yesu yapo wadabwela kuchokela kuchija la a Gelasi wadalandilidwa kwa chimwemwe ndande amatomlindilila.
56 Obala wake adazizwa kupunda, nambho Yesu wadalamula kuti asadamkambila mudhu waliyonjhe pa ivo vachokela.