Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 8

Mwali wa Yailo wahyukichidwa ni wamkazi walamichidwa

40 Yesu yapo wadabwela kuchokela kuchija la a Gelasi wadalandilidwa kwa chimwemwe ndande amatomlindilila. 41 Pamenepo wadafika mundhu mmojhi uyo wamatanidwa Yailo, uyo wadali mchogoleli wa nyumba yophezelana Ayahudi. Wadafika ni kugwada pa miyendo ya Yesu ni kumpembha wapite kukhomo kwake, 42 pakuti mwali wake wayokha wa vyaka ngati khumi ni viwili wadali kudwala pafupi kumwalila.

Yesu yapo wamapita gulu la wandhu amamzenga kupunda. 43 Basi pakati pa gulu la wandhu wajha, padali wamkazi mmojhi uyo wamasusa nghole kwa ndhawi ya vyaka khumi ni viwili, ingakhale wadathowananga chuma chake chonjhe icho wadalinacho kwa masing’anga, nambho palibe uyo wadakhoza kumlamicha. 44 Wamkazi yujha wadajha kumbuyo kwa Yesu ni kugafya njhonga ya chivalo chake, ndhawi imweyo nghole yake idasiya. 45 Yesu wadafunjha, "Yani uyo wanigafya ine?" Wandhu wonjhe adakana. Ni Petulo wadakamba, "Ambuye, ambili akuzungulilani ni kukuzengani!" 46 Nambho Yesu wadakamba, "Pali mundhu wanigafya, najhiwa ndande naona mbhavu zanga zanichoka." 47 Wamkazi yujha yapo wadaona kuti siwakoza kujibisanjho, wadatulukila uku niwatendhemela kwa mandha, wadagwa chifufumimba pamaso pa Yesu. Pamenepo wadafotokoza kwa wandhu wonjhe chifuko cha kumgafyila Yesu ni umo walamichidwila kwankamojhi. 48 Yesu wadamkambila, "Mwali, chikuluphililo chako chakulamicha. Pita kwa mtendele."

49 Yapo Yesu wadali wakali kukamba, wadafika mundhu mmojhi kuchokela kukhomo kwa mchogoleli yujha ni kumkambila Yailo, mchogoleli wa nyumba ya yokomanilana ayahudi, "Mwana wako wamkazi wamwalila, usadayendekela kumsaucha woyaluza." 50 Nambho Yesu yapo wadavela chimwecho wadamkambila Yailo, "Usadaopa, ungokhulupilila, mwali wako siwalame."

51 Yesu yapo wadafika kukhomo kwa Yailo, siwadamulole mundhu ata mmojhi kulowa nawo mnyumba mmenemo ingakale Petulo ni Yohana ni Yakobo ni obala amwali yujha. 52 Ndhawi imeneyo wandhu wonjhe amatolila ni kuimba zaya. Nambho Yesu wadakambila, "Msadalila, pakuti mwali uyu siwadafe, nambho wangogonape!" 53 Anyiiwo adamseka kwa kumdelela, pakuti adajhiwa kuti mwali yujha wamwalila. 54 Nambho Yesu wadamgwila janja mwali yujha ni kukamba, "Mwali, nyakuka!" 55 Umoyo wake udambwelela ni wadanyakuka ndhawi imweyo nikukalanjho wamoyo. Ni Yesu wadakambila obala wake kuti ampache chakudya. 56 Obala wake adazizwa kupunda, nambho Yesu wadalamula kuti asadamkambila mudhu waliyonjhe pa ivo vachokela.

Veja também