Wandhu afuna vizindikilo
38 Ndiipo akumojhi wa oyaluza athauko ni akumojhi a Afalisayo adamkambila Yesu, "Oyaluza, tifuna tione chizindikilo kuchokela kwanu."
39 Yesu wadaayangha, "Mbadwa woipa ni icho chilibe chikhulupililo! Mfuna chizindikilo, nambho simpachidwa chizindikilo nambho chizindikililo chijha cha mlosi Yona. 40 Yona wadakhala masiku ya tatu usiku ni usana mmimba mwa njhomba, nde umo Mwana wa Mundhu siwakhale mkati mwa ndhaka masiku ya tatu usiku ni usana.