Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 15

Yesu waapacha chakudya wandu alufu zinai

32 Ndiipo Yesu wadaatana oyaluzidwa wake ni kwaakambila, "Nililengela lisungu gulu ili la wandhu, ndande yake akhala ni ine kwa masiku yatatu, ni chipano alibe chakudya icho chakhalila. Ine sinifuna kwaalaila akali ni njala, akhoza kukomoka mnjila."

33 Oyaluzidwa wake adaafunjha, "Pano tili ni paphululu, bwanji, sitipate kuti chakudya chokhoza kwaakwanila wandhu wonjhewa?"

34 Yesu wadaafunjha, "Muli ni mabumunda yangati?"

Anyiiwo adayangha, "Mabunda saba ni njhomba zazing’onozingono zochepa."

35 Yesu wadalikambila gulu la wandhu lijha likhale panjhi. 36 Ndiipo wadatenga mabumunda yajha saba ni njhomba zijha, wadamuyamika Mnungu, wadabandula ni kwaapacha oyaluzidwa wake, nawo wadaagawila wajha wandhu. 37 Wandhu wonjhe adadya ni kukhuta. Ndiipo oyaluzidwa wake adakusa vijha vidakhalila nikujhaza miseche saba. 38 Waachimuna yawo adadya adali ngati elufu zinayi, waachikazi ni wana siadawelengedwe.

Veja também