Yesu wakamba kuusu kuvutika ni nyifa yake
21 Kuyambila nyengo imeneyo Yesu wadayamba kuwakambila padanga oyaluzidwa wake, "Nifunika nipite kumujhi wa Yelusalemu, ni kumeneko sinivutichidwe kupunda kupitila mmanja ya waakulu ni akuluakulu wa ajhukulu, ni oyaluza a thauko, ni kumeneko siniphedwe, ni siku la katatu sinihyuke."