3 Ndiipo wadaakambila, "Zene nikukambilani, ngati simng’anamuka ni kulingana ni wana waang’onoang’ono, simulowa mu Ufumu wa kumwamba. 4 Waliyonjhe uyo wajhichepecha ngati mwana uyu, nde uyo siwakhale wamkulu mu Ufumu wa kumwamba. 5 Uyo wamlandila mwana wamng’ono ngati uyu kwa jhina langa, wanilandila ine."