Alendo kuchokela ku dela la kumwela
1 Yesu wadabadwa ku mujhi wa Beselehemu mjhiko la Yudea. Ndhawi imeneyo Helode wadali mfumu. Yesu yapo wadandobadwa wandhu yawo amajhiwa icho sichichokele adafika ku Yelusalemu 2 adaafunjha, "Walikuti mwana uyo wabadwa Mfumu wa Ayahudi? Pakuti tayiona ndhondwa yake kudela la kumwela ni nafenjho tajha kumulambila."