18 "Velani! Tupita ku yelusalemu, kumeneko Mwana wa Mundhu siwapelekedwe kwa wakulu ajhukulu ni oyaluza thauko, anyiiwo siamlamule kuphedwa. 19 Ndiipo saampeleke kwa wandhu yawo osati Ayahudi siamchite chipongwe ni kumkwapula mikwapulo ni siamphe kwa kumpachika pamtanda, ni siku lakatatu siwahyuke."
Publicidade