Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 22

24 "Oyaluza, Musa wadakamba ngati mundhu wammuna wamwalila popande kusiya mwana, mbale wake wamkwate wamkazi wafedwa ni mmunake kuti wambalile mbalewake wana.

30 Wandhu yapo ahyuka palibe kukwata kapena kukwatiwa, siakhale ngati mtumiki wa kumwamba.

Veja também