Pular para o conteúdo
Publicidade

Matayo 27

63 adamkambila, "Imwe ambuye, tikumbukila yujha mundhu wamthila, yapo wadali wakali wa moyo, wadakamba, Sinihyuke siku la katatu.64 Chimwecho lamulani kuti chiliza chilondedwe kwa masiku yatatu. Popande chimwecho oyaluzidwawake akhoza kujha ni kuba thupi lake ni kwakambila wandhu wahyuka. Unami umenewo wothela siukhale woipa kupunda kusiyana ni ujha woyamba."

Veja também