Mchele wa chinyope ni dangalila
13 "Anyiimwe ni mchele wa chinyope wa jhiko. Nambho mchele wa chinyopeo ngati wasukuluka sikomelechedwe ni chiyani? Ulibe njhito. Siutaidwe kubwalo nikupondedwa ni wandhu."
14 "Anyiimwe ni dangalila la jhiko! Ni ngati nyumba iyo yamangidwa pamwamba pa phili siukhoza kubisika.