Nghani za talaka
31 "Idathokambidwanjho, ‘Mundhu waliyonjhe wakafuna kumleka mkazake ifunika wampache talaka.’ 32 Nambho ine nikukambilani mundhu waliyonjhe uyo siwamsiye mkazake kwa ndande yaliyonjhe ijha ni osati kwa ndande ya chigololo wamchita mkazake kukhala wachigololo, ni wammuna waliyonjhe uyo siwamkwate wamkazi uyo wasiidwa nayo wachita chigololo."