2 "Ndiipo yapo umpacha osauka chindhu chilichonjhe usadauzila kwa wandhu. Usadachita ngati agunghuli umo achitila mnyumba yo komanilana Ayahudi ni mnjila kuti wandhu watamande. Zene nikukambilani achameneo atholandila chikho chao chonjhe. 3 Nambho iwe yapo umthangatila osauka chita chimwecho ata mbwenji wako wa pafupi siwadajhiwa. 4 Chindhu chimenecho sichikhale chisisi kwako, Atate wako yao apenya icho wachichita kwa chisisi siakupache chikho."