30 Ngati, Mnungu wayaveka chimwecho machamba ya kuthengo yayo lelo yalipo ni mawa yathilidwa pamoto, bwanji, Mnungu siwakuvekani kupunda anyiimwe? Anyiimwe achikhulupi chochepa!"
31 "Chimwecho, msadajhichaucha nimkamba, ‘Sitidye chiyani! Kapina sitimwe chiyani! Kapina sitivale chiyani!’