Yesu ni Njila yopita kwa Atate
1 Yesu waadakambila, "Simudadandaula mumitima yanu. Mwaakhulupilila Amnungu, munikhulupilile ni ine. 2 Munyumba ya Atate wanga muli ni makhalo yambili, ngati siidakali chimwecho, nidakakukambilani. Chipano nipita kukukonjelani malo. 3 Nikapita kukukonjelani malo, sinibwele kukutengani mujhe kwanga, yapo nili ine namwe mukhalepo.