26 nambho Othandiza, Mzimu woyela, uyo samtume kukhala mmalo mwanga, siwakuyaluzeni kila kandhu ni kukukumbuchani yonjhe yayo nakukambilani."
27 "Mtendele nikusiilani, nikupachani mtendele wanga. Yetu nikupachani osati ngati umo likupachilani jhiko la panjhi. Simudakhaikila mumtima ni simdaopa.