4 Khalani mkati mwanga, ngati umo ine nikhalila mkati mwanu. Ngati umo ndhawi ya mzabibibu siikhoza kubala yokha vipacho popande kukhala mumtengo wa mzabibu, chimwecho anyiimwe simukhoza kuchita chijha achifuna Amnungu ngati simukhala mkati mwanga."
5 "Ine ni mzabibu, anyiimwe ni ndhawi. Yao akhala mkati mwanga, nane nikakhala mkati mwao, achameneo sachite vindhu vabwino vambili, popande ine simukhoza kuchita kandhu.