Yesu wapita ku Nyumba ya Amnungu
13 Phwando la Pasaka la Ayahudi lidawandikila, chimwecho Yesu wadakwela kupita ku Yelusalemu. 14 Ndiipo wadaapheza wandhu mujha mu Nyumba ya Amnungu niaghulicha ng’ombe, mbelele ni nghunda ni ong’anamula ndalama akhala pa gome. 15 Wadakonja mkwapulo wa maluzi, nikwatopola onjhe apite kubwalo pamojhi ni ng’ombe ni mbelele zao, wadataya ndalama za anyiyao amang’anamula ndalama ni kuzigadabula gome zao. 16 Wadakambila anyiwajha amaghulicha nghunda, "Chochani vindhu ivi pano. Simuda chita Nyumba ya Atate wanga kukhala pamalo pa malonda!" 17 Oyaluzidwa wake adakumbukila malembo yayo yalembedwa chimwechi, "Chikondi changa mu Nyumba mwanu siuniphe."