3 Divai yapo idatha, amaye wake adamkambila Yesu, "Divai yatha."
4 Ndiipo Yesu wadayangha amaye wake, "Ndandeyanji munikambila nghani imeneyo. Ndhawi yochita njhito yanga ikali yosafika."
5 Chimwecho amake adazikambila mbowa, "Chilichonjhe icho siwakukambileni, chitani,"