Pular para o conteúdo
Publicidade

Yohana 20

Yesu waachokela oyaluzidwa wake

19 Idali ujhulo siku lo yamba la jhuma. Oyaluzidwa wake adakomana pamojhi mkati mwanyumba, vicheko vidachekedwa ndande ya kwaopa achogoleli wa Ayahudi. Ndiipo Yesu wadajha kuima pakati pao, wadakambila, "Mtendele ukhale kwanu!" 20 Yapo wadakamba yameneyo, wadalangiza manja yake ni ndhiti yake. Chimwechi oyaluzidwa wake adali ni chimwemwe kupunda kwaona Ambuye. 21 Yesu wakambilanjho, "Mtendele ukhale kwanu! Ngati Atate adanituma ine, nane nikutumani anyiimwe." 22 Yapo wadakamba yameneyo, wadaapumbuzila mpuyo ni kwakambila, "Landilani Mzimu Oyela. 23 Mkaalekelela wandhu machimo yao, wandhu achameneo sialekeleledwe, mkasia kwalekelela volakwa vao nawo salekeleledwa."

Veja também