Pular para o conteúdo
Publicidade

Yohana 6

32 Ndiipo Yesu wadakambila, "Zene nikukambilani, osati Musa uyo wadakupachani chakudya kuchoka kumwamba, nambho Atate wanga nde yao akupachani chakudya cha uzene kuchoka kumwamba. 33 Pakuti bumunda la Amnungu nde uyo wachika kuchoka kumwamba ni kwapacha umoyo wandhu a jhiko la panjhi."

34 Ndiipo adamkambila, "Tipache chakudya chimenelo siku zonjhe."

35 Chimwecho wadaakambila, "Ine nde chakudya cha umoyo. Uyo wakujha kwanga siwaona njala ni uyo wanikhulupilila siwaona lujho muyaya.

Veja também