Pular para o conteúdo
Publicidade

João 6

5 Yesu yapo wadapenya ni kuona gulu lalikulu nilimjhela, wadamkambila Filipo, "Sitigule kuti mabumunda yakudya wandhu adye?" 6 Yesu wadakamba chimwecho kwa kumuyesa Filipo, pakuti wadajhiwa icho siwachichite.

7 Ndiipo Filipo wadamuyangha, "Ata ngati tidakhala ni ndalama zochuluka sizikwana kughula chakudya cha kwakwana wandhu anyiyawa, hata ngati kila mmojhi wasiwapachidwe chibandu chaching’onope"

Veja também