Pular para o conteúdo
Publicidade

João 6

53 Ndiipo Yesu wadaakambila, "Zene nikukambilani, mkasiya kudyaa thupi la mwana wa Mundhu ni kumwa mwazi wake, simukhala ni umoyo mkati mwanu. 54 Kila mmojhi uyo siwadye thupi langa ni kumwa mwazi wanga wali ni umoyo wa muyaya, nane sinimuhyuche siku lo thela. 55 Ndande thupi langa nde chakudya cha uzene, ni mwazi wanga nde chakumwa cha uzene. 56 Uyo wakudya thupi langa ni kumwa mwazi wanga, siwakhale mkati mwanga, nane sinikhale mkati mwake. 57 Ngati umo Atate yawo ali amoyo adanitumila, nane nili wamoyo kupitila iwo, chimwecho uyo waniidya ine siwakhale moyo kupitila ine. 58 Chino nde chakudya icho chachika kuchoka kumwamba, osati ngati mana iyo adadya azee wanu, ndiipo adamwalila. Uyo wakudya bumunda lino siwakhale moyo muyaya."

Veja também