3 ndiipo, achabale wake adamkambila, "Uchokepo pano upite ku Yudea dala oyaluzidwa wako azione njhito izo uchita. 4 Mundhu siwachita vindhu ko bisika ngati wafuna kujhiwika ni wandhu. Pakuti uchita vindhu ivi, chipano jhijhiwiche pajhiko la panjhi." 5 Ndande ata achabale wake sadamkhulupilile.